Ekisodo 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+ Salimo 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+
17 Koma ine ndilola Aiguputo kuumitsa mitima yawo,+ kuti atsatire Aisiraeli panyanjapo, kutinso ndipezerepo ulemerero mwa kugonjetsa Farao, magulu ake onse ankhondo, magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi.+
14 Oipa asolola lupanga ndipo akunga uta wawo,+Kuti agwetse osautsika ndi osauka,+Kuti aphe anthu amene njira zawo ndi zowongoka.+