Yobu 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti adzakodwa mu ukonde ndi mapazi ake,Ndipo adzayenda m’zingwe za ukonde.+ Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.] Yeremiya 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Zili choncho, chifukwa pakati pa anthu anga papezeka anthu oipa.+ Iwo amawabisalira ndi kuwayang’anitsitsa ngati mmene wosaka mbalame amachitira.+ Awatchera msampha wowononga pakuti iwo amagwira anthu. Habakuku 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+ Yohane 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu waganyu,+ amene si m’busa ndipo nkhosazo si zake, akaona mmbulu ukubwera amasiya nkhosazo ndi kuthawa, pamenepo mmbuluwo umazigwira ndi kuzibalalitsa,+
5 Anthu odzikweza anditchera msampha.+Iwo aika zingwe ponseponse ngati ukonde m’mphepete mwa njira,+Ndipo anditchera makhwekhwe.+ [Seʹlah.]
26 “‘Zili choncho, chifukwa pakati pa anthu anga papezeka anthu oipa.+ Iwo amawabisalira ndi kuwayang’anitsitsa ngati mmene wosaka mbalame amachitira.+ Awatchera msampha wowononga pakuti iwo amagwira anthu.
15 Mdani amagwira zonsezi ndi mbedza+ ndipo amazikokolola ndi khoka lake n’kuzisonkhanitsa muukonde wake wophera nsomba.+ N’chifukwa chake iye amasangalala ndipo amakhala wokondwa.+
12 Munthu waganyu,+ amene si m’busa ndipo nkhosazo si zake, akaona mmbulu ukubwera amasiya nkhosazo ndi kuthawa, pamenepo mmbuluwo umazigwira ndi kuzibalalitsa,+