Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+ Mika 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+
9 Amadikirira anthu pamalo obisika ngati mkango pamalo ake obisalapo.+Amawadikirira+ kuti atenge mokakamiza munthu wosautsika.Amakulunga wosautsika mu ukonde wake ndi kumutenga mokakamiza.+
2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+