Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+ 1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+ Yeremiya 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+
18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+
6 pamenepo ine ndidzachititsa nyumba iyi kukhala ngati nyumba ya ku Silo.+ Ndipo mzinda uwu ndidzausandutsa chinthu chotembereredwa pakati pa anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi.’”’”+