Salimo 78:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+ Yeremiya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+
60 Pamapeto pake anasiya chihema chopatulika cha ku Silo,+Hema limene anali kukhalamo pakati pa anthu ochokera kufumbi.+
12 “‘Pitani ku Silo,+ kumalo kumene poyamba kunali dzina langa,+ ndipo mukaone zimene ndinachitira malowo chifukwa cha kuipa kwa anthu anga Aisiraeli.+