Deuteronomo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+ Salimo 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu wawala ali ku Ziyoni,+ mzinda wokongola kwambiri.+ Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu wobwezera anthu oipa,+Inu Mulungu wobwezera anthu oipa, walani!+
2 Ndipo anati:“Yehova anafika kuchokera ku Sinai,+Anathwanima pa iwo kuchokera ku Seiri.+Anawala kuchokera kudera lamapiri la Parana,+Ndipo anali ndi miyandamiyanda ya oyera ake,+Kudzanja lake lamanja kunali ankhondo ake.+