Salimo 59:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.] Ezekieli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mkwiyo wanga udzatha+ ndipo ukali wanga ndidzauthetsera pa iwo.+ Kenako mtima wanga udzakhala pansi.+ Ndikadzathetsera ukali wanga pa iwo, pamenepo iwo adzadziwa kuti ine Yehova ndalankhula chifukwa ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha basi.+
13 Afafanizeni mu mkwiyo wanu.+Afafanizeni kuti asakhaleponso.Ndipo adziwe kuti Mulungu akulamulira Yakobo mpaka kumalekezero a dziko lonse lapansi.+ [Seʹlah.]
13 Ndiyeno mkwiyo wanga udzatha+ ndipo ukali wanga ndidzauthetsera pa iwo.+ Kenako mtima wanga udzakhala pansi.+ Ndikadzathetsera ukali wanga pa iwo, pamenepo iwo adzadziwa kuti ine Yehova ndalankhula chifukwa ndimafuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha basi.+