Yeremiya 51:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova. Yohane 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+
39 “Chilakolako chawo chikadzakhala champhavu kwambiri ndidzawakonzera mapwando ndipo ndidzawaledzeretsa kuti asangalale.+ Pamenepo adzagona tulo tomwe tidzakhalapo mpaka kalekale, ndipo sadzadzukanso,”+ watero Yehova.
11 Atanena zimenezi, kenako anauza ophunzira akewo kuti: “Bwenzi lathu Lazaro ali m’tulo akupumula, koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa ku tulo take.”+