Yobu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza. Salimo 95:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwerani timuweramire ndi kumupembedza.+Tiyeni tigwade+ pamaso pa Yehova amene ndiye Wotipanga.+ Salimo 119:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Manja anu anandipanga, ndipo anandiumba.+Ndithandizeni kukhala wozindikira, kuti ndiphunzire malamulo anu.+ Salimo 139:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu munapanga impso zanga,+Ndipo munali kunditchinga m’mimba mwa mayi anga.+ Salimo 149:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Isiraeli asangalale ndi Womupanga Wamkulu,+Ana a Ziyoni akondwere ndi Mfumu yawo.+ Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+ Machitidwe 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu amene anapanga dzikoli ndi zinthu zonse zili mmenemu, sakhala mu akachisi opangidwa ndi manja.+ Iye ndiye Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi.+
8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza.
73 Manja anu anandipanga, ndipo anandiumba.+Ndithandizeni kukhala wozindikira, kuti ndiphunzire malamulo anu.+
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga?+ N’chifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo,+ mwa kuipitsa pangano la makolo athu akale?+
24 Mulungu amene anapanga dzikoli ndi zinthu zonse zili mmenemu, sakhala mu akachisi opangidwa ndi manja.+ Iye ndiye Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi.+