Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+ Salimo 96:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’patseni Yehova ulemerero woyenera dzina lake.+Tengani mphatso ndi kulowa m’mabwalo ake.+
4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+