Salimo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+ Salimo 73:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kwa ine kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+Yehova Ambuye Wamkulu Koposa ndiye pothawirapo panga,+Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+ Salimo 118:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Sindidzafa, koma ndidzakhalabe ndi moyo,+Kuti ndilengeze ntchito za Ya.+
11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+
28 Koma kwa ine kuyandikira kwa Mulungu ndi chinthu chabwino.+Yehova Ambuye Wamkulu Koposa ndiye pothawirapo panga,+Kuti ndilengeze za ntchito zanu zonse.+