Salimo 119:104 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 104 Chifukwa cha malamulo anu ndimachita zinthu mozindikira.+N’chifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+ Salimo 141:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+ Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
104 Chifukwa cha malamulo anu ndimachita zinthu mozindikira.+N’chifukwa chake ndimadana ndi njira iliyonse yachinyengo.+
4 Musachititse mtima wanga kukonda choipa chilichonse,+Kuti ndisamachite zinthu zoipa zonditchukitsa,+Pamodzi ndi amene amachita zinthu zopweteka anzawo,+Kuti ndisadye chakudya chawo chapamwamba.+
8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+