Machitidwe 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mobisa iye anapatula zina mwa ndalamazo n’kusunga, mkazi wakenso anadziwa zimenezo. Ndiyeno anabweretsa zotsalazo n’kudzazipereka kwa atumwi.+ Akolose 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+
2 Koma mobisa iye anapatula zina mwa ndalamazo n’kusunga, mkazi wakenso anadziwa zimenezo. Ndiyeno anabweretsa zotsalazo n’kudzazipereka kwa atumwi.+
8 Koma tsopano zonsezo muzitaye kutali ndi inu.+ Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa, ndi mawu achipongwe,+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+