Salimo 86:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Kukoma mtima kosatha kumene mumawasonyeza onse oitana pa inu ndi kwakukulu.+ Aroma 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chilamulo+ chinalowapo kuti kuchimwa kuonekere kuti ndi kwakukulu.+ Koma pamene uchimo+ unawonjezeka, kukoma mtima kwakukulu+ kunasefukiranso.
5 Pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Kukoma mtima kosatha kumene mumawasonyeza onse oitana pa inu ndi kwakukulu.+
20 Chilamulo+ chinalowapo kuti kuchimwa kuonekere kuti ndi kwakukulu.+ Koma pamene uchimo+ unawonjezeka, kukoma mtima kwakukulu+ kunasefukiranso.