-
Yesaya 61:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndithu ine ndidzakondwera mwa Yehova.+ Moyo wanga udzasangalala ndi Mulungu wanga.+ Pakuti iye wandiveka zovala zachipulumutso.+ Wandiveka malaya akunja achilungamo odula manja,+ ngati mkwati amene wavala chovala chakumutu mofanana ndi wansembe,+ ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.+
-