Salimo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+ Salimo 73:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amanyodola ndi kulankhula zinthu zoipa.+Amalankhula za chinyengo chawo modzikweza.+ Salimo 119:118 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+
14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+
118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+