1 Mafumu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yezebeli mkazi wake anamuuza kuti: “Kodi muziwalamulira chonchi Aisiraeliwa?+ Dzukani, idyani chakudya, mtima wanu usangalale. Ineyo ndikupatsani munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli.”+ Yuda 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu amenewa ndi okonda kung’ung’udza,+ okonda kudandaula za moyo wawo, ongotsatira zilakolako zawo,+ ndipo amalankhula modzitukumula.+ Amatamandanso anthu ena+ n’cholinga choti apezepo phindu.
7 Ndiyeno Yezebeli mkazi wake anamuuza kuti: “Kodi muziwalamulira chonchi Aisiraeliwa?+ Dzukani, idyani chakudya, mtima wanu usangalale. Ineyo ndikupatsani munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli.”+
16 Anthu amenewa ndi okonda kung’ung’udza,+ okonda kudandaula za moyo wawo, ongotsatira zilakolako zawo,+ ndipo amalankhula modzitukumula.+ Amatamandanso anthu ena+ n’cholinga choti apezepo phindu.