Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ Salimo 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+ Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+ Luka 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+
6 Ndithudi, ubwino ndi kukoma mtima kosatha zidzanditsata masiku onse a moyo wanga.+Ndipo ine ndidzakhala m’nyumba ya Yehova mpaka kalekale.+
4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+
37 Tsopano anali mkazi wamasiye,+ ndipo anali ndi zaka 84 koma sanali kusowa pakachisi. Anali kuchita utumiki wopatulika usana ndi usiku,+ anali kusala kudya ndi kupereka mapembedzero.