Salimo 88:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira pa unyamata wanga ndakhala ndikusautsika komanso kutsala pang’ono kufa.+Ndapirira kwambiri zinthu zoopsa zochokera kwa inu.+ Miyambo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+
15 Kuyambira pa unyamata wanga ndakhala ndikusautsika komanso kutsala pang’ono kufa.+Ndapirira kwambiri zinthu zoopsa zochokera kwa inu.+
13 Mtima wachimwemwe umapangitsa nkhope kusangalala,+ koma chifukwa cha kupweteka kwa mtima munthu sasangalala.+