Ekisodo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukamuzunza ngakhale pang’ono, iye n’kundilirira, ndidzamva ndithu kulira kwake.+ Deuteronomo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+ Salimo 68:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+
19 “‘Wotembereredwa ndi munthu wopotoza+ chiweruzo+ cha mlendo wokhala pakati panu,+ mwana wamasiye* ndi mkazi wamasiye.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)
14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+
5 Tate wa ana amasiye* ndi woweruzira akazi amasiye milandu,+Ndi Mulungu amene amakhala m’malo ake oyera.+