Miyambo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+
11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+