Salimo 91:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzakunyamula m’manja mwawo,+Kuti phazi lako lisawombe mwala uliwonse.+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+Amene amakuyang’anira sangawodzere.+ Miyambo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ukamayenda, sudzayenda mopanikizika+ ndipo ngati ukuthamanga sudzapunthwa.+ Yesaya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+
7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.+ Popeza inu ndinu wochita zowongoka, mudzasalaza njira ya munthu wolungama.+