Miyambo 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ukatero udzayenda panjira yako popanda chokuopseza,+ ndipo ngakhale phazi lako silidzapunthwa ndi chilichonse.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+ Yohane 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu anayankha kuti: “Kodi usana suli ndi maola 12? Munthu akayenda masana+ palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.
23 Ukatero udzayenda panjira yako popanda chokuopseza,+ ndipo ngakhale phazi lako silidzapunthwa ndi chilichonse.+
31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+
9 Yesu anayankha kuti: “Kodi usana suli ndi maola 12? Munthu akayenda masana+ palibe chimamupunthwitsa, chifukwa amaona kuwala kwa dzikoli.