Salimo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Yesaya 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo.+ Ndimadana ndi zauchifwamba ndi kupanda chilungamo.+ Ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,+ ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+
5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
8 Pakuti ine Yehova ndimakonda chilungamo.+ Ndimadana ndi zauchifwamba ndi kupanda chilungamo.+ Ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,+ ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+