Miyambo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pali zinthu 6 zimene Yehova amadana nazo.+ Zilipo zinthu 7 zimene moyo wake umanyansidwa nazo:+ Yeremiya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+ Zekariya 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.” Malaki 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.
9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+
17 Musamakonzerane ziwembu mumtima mwanu kuti muonetsane tsoka+ ndipo musamakonde kulumbira monama.+ Pakuti zinthu zonsezi ine ndimadana nazo,’+ watero Yehova.”
8 “Kodi munthu wochokera kufumbi angabere Mulungu? Komatu inu mukundibera.” Inu mukunena kuti: “Takuberani motani?” “Mukundibera kudzera m’chakhumi* ndi m’zopereka.