Genesis 39:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo mkaziyo anam’gwira malaya+ mnyamatayo n’kumuuza kuti: “Ugone nane basi!”+ Koma mnyamatayo anangovula malayawo n’kuwasiya m’manja mwa mkaziyo n’kuthawira panja.+ Chivumbulutso 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Komabe, ndakupeza ndi mlandu uwu. Walekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadzitcha mneneri. Iye amaphunzitsa+ ndi kusocheretsa akapolo anga+ kuti azichita dama+ ndi kudya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano.+
12 Pamenepo mkaziyo anam’gwira malaya+ mnyamatayo n’kumuuza kuti: “Ugone nane basi!”+ Koma mnyamatayo anangovula malayawo n’kuwasiya m’manja mwa mkaziyo n’kuthawira panja.+
20 “‘Komabe, ndakupeza ndi mlandu uwu. Walekerera mayi uja Yezebeli,+ amene amadzitcha mneneri. Iye amaphunzitsa+ ndi kusocheretsa akapolo anga+ kuti azichita dama+ ndi kudya zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano.+