Miyambo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amayang’anira pakamwa pake amasunga moyo wake.+ Amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+ Miyambo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakamwa pa munthu wopusa m’pamene pamamuwononga,+ ndipo milomo yake ndi msampha wa moyo wake.+ Miyambo 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wosunga pakamwa pake ndiponso lilime lake akuteteza moyo wake ku masautso.+
3 Amene amayang’anira pakamwa pake amasunga moyo wake.+ Amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+