Deuteronomo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+ 1 Samueli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+Wotsitsa ndiponso Wokweza,+ Salimo 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu amene Mulungu akuwadalitsa adzalandira dziko lapansi,+Koma amene wawatemberera adzaphedwa.+ Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa moti amachuluka kwambiri,+Ndipo salola kuti ng’ombe zawo zikhale zochepa.+
18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+
7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+Wotsitsa ndiponso Wokweza,+ Salimo 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu amene Mulungu akuwadalitsa adzalandira dziko lapansi,+Koma amene wawatemberera adzaphedwa.+ Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa moti amachuluka kwambiri,+Ndipo salola kuti ng’ombe zawo zikhale zochepa.+