Miyambo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amene amachulukitsa zinthu zamtengo wapatali kuchokera ku chiwongoladzanja ndi katapira,*+ amangosungira zinthuzo munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+ Mlaliki 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chumacho chimatha+ chifukwa cha zoipa zinazake zimene zachitika, kenako iye amabereka mwana wamwamuna pamene alibe chilichonse choti angapatse mwanayo ngati cholowa.+ Yeremiya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+
8 Munthu amene amachulukitsa zinthu zamtengo wapatali kuchokera ku chiwongoladzanja ndi katapira,*+ amangosungira zinthuzo munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+
14 Chumacho chimatha+ chifukwa cha zoipa zinazake zimene zachitika, kenako iye amabereka mwana wamwamuna pamene alibe chilichonse choti angapatse mwanayo ngati cholowa.+
11 Munthu wopeza chuma mopanda chilungamo+ ali ngati nkhwali imene yasonkhanitsa mazira amene sinaikire. Chuma chakecho adzachisiya asanakwanitse ngakhale hafu ya zaka za moyo wake,+ ndipo pamapeto pake adzaonekera kuti ndi wopusa.”+