Salimo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso mtumiki wanu amachenjezedwa nazo.+Munthu wosunga zigamulozo amapeza mphoto yaikulu.+ 2 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+
8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+