Miyambo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+ Miyambo 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+ 2 Akorinto 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ponena za nkhaniyi, wobzala moumira+ adzakololanso zochepa, ndipo wobzala mowolowa manja+ adzakololanso zochuluka.
11 Wolima nthaka yake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+ koma wofunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru mumtima mwake.+
18 Amene akuteteza mtengo wa mkuyu adzadya zipatso zake,+ ndipo amene akuteteza mbuye wake adzalemekezedwa.+
6 Koma ponena za nkhaniyi, wobzala moumira+ adzakololanso zochepa, ndipo wobzala mowolowa manja+ adzakololanso zochuluka.