Miyambo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yokhulupirika ndi imene sinama,+ koma mboni yonyenga imanena bodza lokhalokha.+ 1 Timoteyo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zimenezi zidzachitikanso chifukwa cha chinyengo cha anthu olankhula mabodza,+ amene chikumbumtima chawo chili ngati chipsera+ chobwera chifukwa chopsa ndi chitsulo chamoto. 2 Timoteyo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu amenewa apatuka pa choonadi,+ ponena kuti kuuka kwa akufa kunachitika kale+ ndipo akuwononga chikhulupiriro cha ena.+
2 Zimenezi zidzachitikanso chifukwa cha chinyengo cha anthu olankhula mabodza,+ amene chikumbumtima chawo chili ngati chipsera+ chobwera chifukwa chopsa ndi chitsulo chamoto.
18 Anthu amenewa apatuka pa choonadi,+ ponena kuti kuuka kwa akufa kunachitika kale+ ndipo akuwononga chikhulupiriro cha ena.+