Levitiko 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Muzikhala ndi masikelo olondola,+ miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu, muyezo wolondola wa efa ndi muyezo wolondola wa hini.* Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo. Miyambo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Sikelo yachinyengo imam’nyansa Yehova,+ koma mwala woyezera, wolemera mokwanira, umam’sangalatsa. Ezekieli 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Anthu inu muzikhala ndi masikelo olondola, muyezo wa efa* wolondola ndi mitsuko* yoyezera yolondola.+
36 Muzikhala ndi masikelo olondola,+ miyala yolondola yoyezera kulemera kwa zinthu, muyezo wolondola wa efa ndi muyezo wolondola wa hini.* Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.
10 ‘Anthu inu muzikhala ndi masikelo olondola, muyezo wa efa* wolondola ndi mitsuko* yoyezera yolondola.+