1 Samueli 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+ 2 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+ Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+ Yohane 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+
3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+
26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+
24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+
13 Palibe amene ali ndi chikondi chachikulu kuposa cha munthu amene wapereka moyo wake chifukwa cha mabwenzi ake.+