2 Mafumu 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atatero, analowa m’nyumba ndipo anayamba kudya ndi kumwa, kenako anati: “Amuna inu, m’samaleni munthu wotembereredwayu.+ M’tengeni mukamuike m’manda, popeza ndi mwana wa mfumu.”+ 2 Mbiri 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mumzinda, ku Yerusalemu. Iye sanaikidwe m’manda a mafumu a Isiraeli.+ Kenako Hezekiya mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
34 Atatero, analowa m’nyumba ndipo anayamba kudya ndi kumwa, kenako anati: “Amuna inu, m’samaleni munthu wotembereredwayu.+ M’tengeni mukamuike m’manda, popeza ndi mwana wa mfumu.”+
27 Pomalizira pake, Ahazi anagona pamodzi ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda mumzinda, ku Yerusalemu. Iye sanaikidwe m’manda a mafumu a Isiraeli.+ Kenako Hezekiya mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.