Salimo 37:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+ Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+
30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+
2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+