Genesis 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+ Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
27 n’kunena kuti: “Atamandike Yehova,+ Mulungu wa mbuyanga Abulahamu, amene sanasiye kusonyeza mbuyanga kukoma mtima kosatha ndi kukhala wokhulupirika kwa iye. Pa ulendo wangawu, Yehova wanditsogolera kunyumba kwa abale a mbuyanga.”+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+