1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+ Salimo 82:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani inu Mulungu, weruzani dziko lapansi.+Pakuti inu nokha muyenera kutenga mitundu yonse kukhala yanu.+ Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Salimo 110:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
10 Onse olimbana ndi Yehova adzagwidwa ndi mantha.+Motsutsana nawo, iye adzagunda ngati mabingu kumwamba.+Yehova mwiniwake adzaweruza dziko lonse lapansi,+Kuti apereke mphamvu kwa mfumu yake,+Ndi kuti akweze nyanga ya wodzozedwa wake.”+
8 Nyamukani inu Mulungu, weruzani dziko lapansi.+Pakuti inu nokha muyenera kutenga mitundu yonse kukhala yanu.+
13 Pakuti iye wabwera.+Iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+Adzaweruza dziko mwachilungamo,+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”