2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Yesaya 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri udzatsala wokhawokha. Malo odyetserako ziweto adzakhala opanda kanthu ndipo adzasiyidwa ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ng’ombe azidzadya msipu ndipo azidzagona pansi. Iye adzadya nthambi zake.+
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
10 Pakuti mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri udzatsala wokhawokha. Malo odyetserako ziweto adzakhala opanda kanthu ndipo adzasiyidwa ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ng’ombe azidzadya msipu ndipo azidzagona pansi. Iye adzadya nthambi zake.+