Levitiko 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+ Salimo 119:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzakonda malamulo anu.+Ndipo sindidzaiwala mawu anu.+ Yakobo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu wopereka lamulo ndi woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani, kuti uziweruza mnzako?+
15 “Mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu ndi kuonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi mfundo zake zimene ndikukupatsani lero, matemberero otsatirawa adzakugwerani ndi kukupezani:+
12 Komatu wopereka lamulo ndi woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani, kuti uziweruza mnzako?+