Salimo 39:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.] Salimo 144:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Munthu amafanana ndi mpweya wotuluka m’mphuno.+Masiku ake ali ngati mthunzi wongodutsa.+ Yesaya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+
11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.]
11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+