Salimo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wokhala kumwamba+ adzaseka,Yehova adzawanyodola.+ Salimo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+ Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+ Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+
33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+