Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndi mpando wanga wachifumu ndipo dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga.+ Ndiye kodi mungandimangire nyumba yotani,+Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo ali kuti?”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 49 Yesaya 2, ptsa. 390-392 Nsanja ya Olonda,6/15/1998, tsa. 128/15/1991, tsa. 138/15/1989, ptsa. 15-16
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndi mpando wanga wachifumu ndipo dziko lapansi ndi chopondapo mapazi anga.+ Ndiye kodi mungandimangire nyumba yotani,+Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo ali kuti?”+
66:1 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 49 Yesaya 2, ptsa. 390-392 Nsanja ya Olonda,6/15/1998, tsa. 128/15/1991, tsa. 138/15/1989, ptsa. 15-16