Ekisodo 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova ndi wankhondo.+ Dzina lake ndi Yehova.+ Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+