Deuteronomo 32:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+ Mika 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzabwezera mokwiya ndiponso mwaukali mitundu ya anthu imene sinandimvere.”+ Aroma 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Olamulirawo ndi mtumiki wa Mulungu kuti zinthu zikuyendere bwino.+ Koma ngati ukuchita zoipa,+ chita mantha chifukwa sagwira lupanga pachabe, pakuti iye ndi mtumiki wa Mulungu wosonyeza mkwiyo wa Mulungu kwa munthu wochita zoipa.+ Aheberi 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+
35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+
4 Olamulirawo ndi mtumiki wa Mulungu kuti zinthu zikuyendere bwino.+ Koma ngati ukuchita zoipa,+ chita mantha chifukwa sagwira lupanga pachabe, pakuti iye ndi mtumiki wa Mulungu wosonyeza mkwiyo wa Mulungu kwa munthu wochita zoipa.+
30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+