Salimo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+ Yesaya 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Yehova, amene anawombola Abulahamu, wanena izi kwa nyumba ya Yakobo:+ “Tsopano Yakobo sachita manyazi. Tsopano nkhope yake sikhala yakugwa,+ Yoweli 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo mudzadya ndi kukhuta+ ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu+ amene wakuchitirani zodabwitsa.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.*+
3 Ndithudi, palibe aliyense amene adzachita manyazi mwa anthu amene chiyembekezo chawo chili mwa inu.+Amene adzachite manyazi ndi amene akuchita zinthu mwachinyengo koma osaphula kanthu.+
22 Chotero Yehova, amene anawombola Abulahamu, wanena izi kwa nyumba ya Yakobo:+ “Tsopano Yakobo sachita manyazi. Tsopano nkhope yake sikhala yakugwa,+
26 Pamenepo mudzadya ndi kukhuta+ ndipo mudzatamanda dzina la Yehova Mulungu wanu+ amene wakuchitirani zodabwitsa.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.*+