Levitiko 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+ Deuteronomo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 yokhalanso ndi nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino zimene sunaikemo ndiwe, ndi zitsime* zimene sunakumbe ndiwe, minda ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene sunabzale ndiwe, n’kudya ndi kukhuta,+ Salimo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ofatsa adzadya ndi kukhuta.+Ofunafuna Yehova adzamutamanda.+Mitima yanu ikhale ndi moyo kosatha.+
5 Pamenepo, mudzakhala mukupuntha zimene mwakolola kufikira nyengo yokolola mphesa, ndipo mudzakhala mukukolola mphesa kufikira nyengo yofesa mbewu. Mudzadya mkate wanu ndi kukhuta,+ ndipo mudzakhala otetezeka m’dziko lanu.+
11 yokhalanso ndi nyumba zodzaza ndi zinthu zonse zabwino zimene sunaikemo ndiwe, ndi zitsime* zimene sunakumbe ndiwe, minda ya mpesa ndi mitengo ya maolivi imene sunabzale ndiwe, n’kudya ndi kukhuta,+