Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+ Nehemiya 9:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+ Yesaya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lanu lawonongedwa.+ Mizinda yanu yatenthedwa ndi moto,+ ndipo alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Chilichonse chawonongeka ngati mmene zimakhalira adani akalanda dziko.+ Maliro 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Cholowa chathu chaperekedwa kwa anthu achilendo. Nyumba zathu zaperekedwa kwa alendo.+ Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+
33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+
37 Zokolola za m’dzikoli zachulukira+ mafumu+ amene mwatiikira chifukwa cha machimo athu.+ Iwo akulamulira matupi athu komanso ziweto zathu mmene akufunira, ndipo tili pamavuto aakulu.+
7 Dziko lanu lawonongedwa.+ Mizinda yanu yatenthedwa ndi moto,+ ndipo alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Chilichonse chawonongeka ngati mmene zimakhalira adani akalanda dziko.+
7 “Iwo akungofesa mphepo, ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Tirigu amene ali m’minda yawo sakukula.+ Mbewu zawo sizikuwapatsa ufa.+ Ngati zina mwa mbewuzo zingabereke, alendo adzazimeza.+