23 Anthu a mitundu ina adzadziwa kuti a nyumba ya Isiraeli anatengedwa kupita ku ukapolo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Adzadziwa kuti anali kundichitira zinthu zosakhulupirika. N’chifukwa chake ine ndinawabisira nkhope yanga+ n’kuwapereka m’manja mwa adani awo ndipo onsewo anaphedwa ndi lupanga.+