5 Kodi si mmene nyumba yanga ilili kwa Mulungu?+
Chifukwa chakuti anachita nane pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+
Analikonza bwino ndipo n’lotetezeka.+
Chifukwa ndilo chipulumutso changa+ ndi chondikondweretsa,
Kodi chimenechi sindicho chifukwa chake adzakulitsa panganoli?+